Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 8:34 - Buku Lopatulika

34 Monga anachita lero lino, momwemo Yehova analamula kuchita, kukuchitirani chotetezera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Monga anachita lero lino, momwemo Yehova anauza kuchita, kukuchitirani chotetezera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Chauta adatilamula kuti tikuchiteni zimene takuchitanizi, kuti ukhale mwambo wopepesera machimo anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Zimene zachitika lerozi analamula ndi Yehova kuti zichitike ngati nsembe yopepesera machimo anu.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 8:34
5 Mawu Ofanana  

Ndipo musatuluka pa khomo la chihema chokomanako masiku asanu ndi awiri, kufikira anakwanira masiku a kudzaza manja kwanu; pakuti adzaze manja anu masiku asanu ndi awiri.


Ndipo mukhale pakhomo pa chihema chokomanako masiku asanu ndi awiri, usana ndi usiku, ndi kusunga chilangizo cha Yehova, kuti mungafe; pakuti anandiuza kotero.


amene wakhala si monga mwa lamulo la lamuliro la kwa thupi, komatu monga mwa mphamvu ya moyo wosaonongeka;


amene alibe chifukwa cha kupereka nsembe tsiku ndi tsiku monga akulu a ansembe, yoyambira chifukwa cha zoipa za iwo eni, yinayi chifukwa cha zoipa za anthu; pakuti ichi anachita kamodzi, kwatha, podzipereka yekha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa