Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 8:32 - Buku Lopatulika

32 Koma chotsalira cha nyama ndi mkate muchitenthe ndi moto.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Koma chotsalira cha nyama ndi mkate muchitenthe ndi moto.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Zotsala zake za nyamayo ndi za buledi zomwe, muzitenthe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ndipo nyama ndi buledi zotsalazo, muziwotche.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 8:32
8 Mawu Ofanana  

Ndipo musasiyako kufikira m'mawa; koma yotsalira kufikira m'mamawayo muipsereze ndi moto.


Ndipo ikatsalako nyama yodzaza manja, kapena mkate kufikira m'mawa, pamenepo utenthe zotsalazo ndi moto; asazidye popeza nchopatulika ichi.


Usanyadire zamawa, popeza sudziwa tsiku lina lidzabala chiyani?


Chilichonse dzanja lako lichipeza kuchichita, uchichite ndi mphamvu yako; pakuti mulibe ntchito ngakhale kulingirira ngakhale kudziwa, ngakhale nzeru, kumanda ulikupitako.


koma chotsalira pa nyama ya nsembeyo tsiku lachitatu, achitenthe.


Ndipo musatuluka pa khomo la chihema chokomanako masiku asanu ndi awiri, kufikira anakwanira masiku a kudzaza manja kwanu; pakuti adzaze manja anu masiku asanu ndi awiri.


(pakuti anena, M'nyengo yolandiridwa ndinamva iwe, ndipo m'tsiku la chipulumutso ndinakuthandiza. Taonani, tsopano ndiyo nyengo yabwino yolandiridwa, taonani, tsopano ndilo tsiku la chipulumutso);


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa