Levitiko 8:26 - Buku Lopatulika26 ndipo mu dengu la mkate wopanda chotupitsa wokhala pamaso pa Yehova, anatengeramo kamtanda kamodzi kopanda chotupitsa, ndi kamtanda kamodzi ka mkate wamafuta, ndi kamtanda kamodzi kaphanthi, natiika pa mafutawo, ndi pa mwendo wathako wa ku dzanja lamanja; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndipo mu dengu la mkate wopanda chotupitsa wokhala pamaso pa Yehova, anatengeramo kamtanda kamodzi kopanda chotupitsa, ndi kamtanda kamodzi ka mkate wamafuta, ndi kamtanda kamodzi kaphanthi, natiika pa mafutawo, ndi pa mwendo wathako wa ku dzanja lamanja; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Ndipo m'dengu la buledi wosafufumitsa, lopatulikira Chauta, adatengamo mtanda umodzi wa buledi wosafufumitsa, mtanda umodzi adatengamo mtanda umodzi wa buledi wosafufumitsa, mtanda umodzi wopaka mafuta ndi mtanda umodzi wa buledi wopyapyala. Zonsezo ataziika pa mafuta aja ndi pa ntchafu ya ku dzanja lamanja ija, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ndipo mʼdengu la buledi wopanda yisiti limene linali pamaso pa Yehova, anatengamo buledi mmodzi, buledi mmodzi wokhala ndi mafuta a olivi, ndi buledi wopyapyala mmodzi. Zonsezi anaziyika pa mafuta aja ndi pa ntchafu ya ku dzanja lamanja ija. Onani mutuwo |