Levitiko 8:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo anapadzula mphongoyo ziwalo zake; ndi Mose anatentha mutuwo ndi ziwalo, ndi mafuta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo anapadzula mphongoyo ziwalo zake; ndi Mose anatentha mutuwo ndi ziwalo, ndi mafuta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Atadula nkhosayo nthulinthuli, Mose adatentha mutu wake ndi nthuli zija ndi mafuta ake omwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Anayidula nkhosayo nthulinthuli ndipo anatentha mutu wake, nthulizo ndi mafuta. Onani mutuwo |