Levitiko 8:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo anaipha; ndi Mose anawaza mwazi wake paguwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo anaipha; ndi Mose anawaza mwazi wake pa guwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Kenaka Mose adaipha nathira magazi ake pa guwa mozungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ndipo Mose anapha nkhosayo ndi kuwaza magazi ake mbali zonse zaguwalo. Onani mutuwo |