Levitiko 8:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anabwera nayo nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza; ndipo Aroni ndi ana ake aamuna anaika manja ao pamutu pa mphongoyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anabwera nayo nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza; ndipo Aroni ndi ana ake amuna anaika manja ao pamutu pa mphongoyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambuyo pake adapereka nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza, ndipo Aroni ndi ana ake adasanjika manja ao pamutu pa nkhosayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka anabwera ndi nkhosa yayimuna ya nsembe yopsereza, ndipo Aaroni ndi ana ake aamuna anasanjika manja awo pamutu pake. Onani mutuwo |