Levitiko 8:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anatenga mafuta onse a pamatumbo, ndi chokuta cha mphafa, ndi impso ziwiri, ndi mafuta ake, ndipo Mose anazitentha paguwa la nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anatenga mafuta onse a pamatumbo, ndi chokuta cha mphafa, ndi impso ziwiri, ndi mafuta ake, ndipo Mose anazitentha pa guwa la nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono Mose adatenga mafuta onse akumatumbo ndi mphumphu ya mafuta akuchiŵindi, ndi imso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe, ndipo adazitenthera paguwapo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mose anatenganso mafuta onse okuta matumbo, mafuta ophimba chiwindi, ndiponso impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta ake, nazitentha pa guwapo. Onani mutuwo |