Levitiko 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Mose anatenga mafuta odzoza, nadzoza chihema, ndi zonse zili m'mwemo, nazipatula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Mose anatenga mafuta odzoza, nadzoza Kachisi, ndi zonse zili m'mwemo, nazipatula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pambuyo pake Mose adatenga mafuta odzozera, nadzoza chihema chamsonkhano pamodzi ndi zonse zimene zinali m'menemo, ndipo adazipatula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamenepo Mose anatenga mafuta wodzozera nadzoza tenti ya msonkhano pamodzi ndi zonse zimene zinali mʼmenemo, ndipo potero anazipatula. Onani mutuwo |