Levitiko 7:29 - Buku Lopatulika29 Lankhula ndi ana a Israele, ndi kuti, Wakubwera nayo nsembe yoyamika yake kwa Yehova, azidza nacho chopereka chake kwa Yehova chochokera ku nsembe yoyamika yake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Lankhula ndi ana a Israele, ndi kuti, Wakubwera nayo nsembe yoyamika yake kwa Yehova, azidza nacho chopereka chake kwa Yehova chochokera ku nsembe yoyamika yake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 “Uza Aisraele kuti, ‘Munthu amene apereka nsembe yake yachiyanjano kwa Chauta, abwere ndi gawo la nsembeyo kwa Chauta. Pa nsembe yake yachiyanjanoyo Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 “Awuze Aisraeli kuti, Aliyense amene apereka nsembe yachiyanjano kwa Yehova, abwere ndi gawo la nsembeyo kwa Yehova. Onani mutuwo |