Levitiko 6:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo adze nayo nsembe yake yopalamula kwa Yehova, ndiyo nkhosa yamphongo yopanda chilema ya m'khola mwake, monga umayesa mtengo wake, ikhale nsembe yopalamula, adze nayo kwa wansembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo adze nayo nsembe yake yopalamula kwa Yehova, ndiyo nkhosa yamphongo yopanda chilema ya m'khola mwake, monga umayesa mtengo wake, ikhale nsembe yopalamula, adze nayo kwa wansembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndipo nsembe yopepesera kupalamula, yopereka kwa Chauta, abwere nayo kwa wansembe. Ikhale nkhosa yamphongo yopanda chilema, mtengo wake wa nkhosayo ukhale wokwanira mtengo woikidwa wa nyama ya nsembe yopepesera kupalamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pambuyo pake apereke kwa Yehova nsembe yopalamula. Nsembe yake ikhale nkhosa yayimuna yopanda chilema ndipo mtengo wake wogwirizana ndi nsembe yopepesera machimo. Onani mutuwo |