Levitiko 5:5 - Buku Lopatulika5 ndipo kudzali, atapalamula chimodzi cha izi, aziwulula chimene adachimwa nacho; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 ndipo kudzali, atapalamula chimodzi cha izi, aziwulula chimene adachimwa nacho; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Munthu akapalamula pa chilichonse mwa zimene tatchulazi, aulule tchimo lakelo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “ ‘Pamene munthu wazindikira kuti wachimwa motere, awulule tchimo limene wachitalo. Onani mutuwo |