Levitiko 5:18 - Buku Lopatulika18 Nadze nayo kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema ya m'khola lake, monga umayesa mtengo wake, ikhale nsembe yopalamula; ndipo wansembeyo amchitire chomtetezera chifukwa cha kusachimwa dala kwake, osakudziwa; ndipo adzakhululukidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nadze nayo kwa wansembe nkhosa yamphongo yopanda chilema ya m'khola lake, monga umayesa mtengo wake, ikhale nsembe yopalamula; ndipo wansembeyo amchitire chomtetezera chifukwa cha kusachimwa dala kwake, osakudziwa; ndipo adzakhululukidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Abwere kwa wansembe ndi nkhosa yamphongo yopanda chilema, imene mtengo wake ulingane ndi wa nyama ya nsembe yopepesera kupalamula. Wansembeyo achite mwambo wopepesera machimo amene munthuyo adachita mosadziŵawo, ndipo wochimwayo adzakhululukidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Abwere kwa wansembe ndi chopereka chopepesera kupalamula kwake. Chopereka chikhale nkhosa yayimuna yopanda chilema ndipo mtengo wake ukhale woyenera nsembe yopepesera kupalamula kumene anachimwa mosadziwako, ndipo munthuyo adzakhululukidwa. Onani mutuwo |