Levitiko 4:14 - Buku Lopatulika14 kukadziwika kuchimwa adachimwako, pamenepo msonkhano uzibwera nayo ng'ombe yamphongo, ikhale nsembe yauchimo, ndipo udze nayo ku khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 kukadziwika kuchimwa adachimwako, pamenepo msonkhano uzibwera nayo ng'ombe yamphongo, ikhale nsembe yauchimo, ndipo udze nayo ku khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono tchimo lakelo nkudziŵika, mpingo wonsewo upereke ng'ombe yaing'ono yamphongo kuti ikhale nsembe yopepesera machimo, ndipo abwere nayo pa khomo la chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Akazindikira tchimo limene achita, gulu lonse lipereke mwana wangʼombe wamphongo kuti akhale chopereka chopepesera tchimo ndipo abwere naye pa khomo la tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |