Levitiko 3:15 - Buku Lopatulika15 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo, okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Apatulenso imso ziŵiri pamodzi ndi mafuta ake omwe cham'chiwunomu, ndiponso mphumphu ya mafuta akuchiŵindi, ochotsa pamodzi ndi imso zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta onse omwe akuta impsyozo ndi msonga ya chiwindi imene adzachotsera pamodzi ndi impsyo zija. Onani mutuwo |