Levitiko 3:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo abwere nacho chopereka chake chotengako, ndicho nsembe yamoto ya kwa Yehova; achotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo abwere nacho chopereka chake chotengako, ndicho nsembe yamoto ya kwa Yehova; achotse mafuta akukuta matumbo, ndi mafuta onse akukhala pamatumbo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono pa nsembe yopereka kwa Chautayo ndipo yoyenera kuitentha pa moto, atapepo mafuta okuta matumbo ndi mafuta ena onse okhala pamatumbopo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsono pa nsembe yoti iwotchedwe kukhala nsembe chakudya ya Yehova, achotse ndi kubweretsa: mafuta onse amene amaphimba zamʼkati kapena mafuta onse a mʼkatimo, Onani mutuwo |