Levitiko 3:13 - Buku Lopatulika13 naike dzanja lake pamutu pake, naiphe pa khomo la chihema chokomanako; ndipo ana a Aroni awaze mwazi wake paguwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 naike dzanja lake pamutu pake, naiphe pa khomo la chihema chokomanako; ndipo ana a Aroni awaze mwazi wake pa guwa la nsembe pozungulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Asanjike dzanja lake pamutu pa mbuziyo, ndipo aiphere pakhomo pa chihema chamsonkhano. Pambuyo pake ana a Aroni aliwaze magazi guwa molizungulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Asanjike dzanja lake pamutu pa mbuziyo ndipo ayiphere pa khomo la tenti ya msonkhano. Ndipo ana a Aaroni awaze magazi ake mbali zonse za guwa. Onani mutuwo |