Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 27:7 - Buku Lopatulika

7 Akakhala munthu wa zaka makumi asanu ndi limodzi ndi mphambu, akakhala wamwamuna, umuyesere wa masekeli khumi ndi asanu, akakhala wamkazi wa masekeli khumi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Akakhala munthu wa zaka makumi asanu ndi limodzi ndi mphambu, akakhala wamwamuna, umuyesere wa masekeli khumi ndi asanu, akakhala wamkazi wa masekeli khumi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Munthu wake akakhala wa zaka 60 kapena kupitirirapo, mtengo wake ukhale wokwana masekeli asiliva 15 pa munthu wamwamuna, ndipo khumi pa munthu wamkazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ngati ndi munthu wa zaka makumi asanu ndi limodzi kapena kuposerapo, mtengo wa wamwamuna ukhale masekeli khumi ndi asanu, ndipo wamkazi ukhale masekeli khumi.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 27:7
3 Mawu Ofanana  

Masiku a zaka zathu ndiwo zaka makumi asanu ndi awiri, kapena tikakhala nayo mphamvudi zaka makumi asanu ndi atatu; koma teronso kukula kwao kumati chivuto ndi chopanda pake; pakuti kumapitako msanga ndipo tithawa ife tomwe.


Akakhala mwana wa mwezi umodzi kufikira zaka zisanu, uziwayesera wamwamuna wa masekeli asanu a siliva, ndi wamkazi wa masekeli atatu a siliva.


Koma chuma chake chikapanda kufikira kuyesa kwako, amuike pamaso pa wansembe, kuti wansembeyo amuyese; ndipo wansembeyo amuyese, monga akhoza iye amene anawinda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa