Levitiko 27:6 - Buku Lopatulika6 Akakhala mwana wa mwezi umodzi kufikira zaka zisanu, uziwayesera wamwamuna wa masekeli asanu a siliva, ndi wamkazi wa masekeli atatu a siliva. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Akakhala mwana wa mwezi umodzi kufikira zaka zisanu, uziwayesera wamwamuna wa masekeli asanu a siliva, ndi wamkazi wa masekeli atatu a siliva. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Akakhala munthu wa mwezi umodzi mpaka zaka zisanu, mtengo wake ukhale wokwana mashekeli asiliva zisanu pa munthu wamwamuna, ndipo zitatu pa munthu wamkazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ngati ndi munthu wamwamuna wa pakati pa mwezi umodzi ndi zaka zisanu, mtengo wa munthu wamwamuna ukhale masekeli asanu a siliva ndipo ngati ndi wamkazi, ukhale masekeli atatu a siliva. Onani mutuwo |