Levitiko 27:34 - Buku Lopatulika34 Awa ndi malamulo, amene Yehova analamula Mose, awauze ana a Israele, m'phiri la Sinai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Awa ndi malamulo, amene Yehova anauza Mose, awauze ana a Israele, m'phiri la Sinai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Ameneŵa ndiwo malamulo amene Chauta adalamula Mose pa phiri la Sinai kuti auze Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Amenewa ndi malamulo amene Yehova anamupatsa Mose pa Phiri la Sinai kuti awuze Aisraeli. Onani mutuwo |