Levitiko 27:24 - Buku Lopatulika24 Chaka choliza lipenga mundawo ubwerere kwa iye amene adaugulitsa, kwa iye amene dzikoli ndi lakelake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Chaka choliza lipenga mundawo ubwerere kwa iye amene adaugulitsa, kwa iye amene dzikoli ndi lakelake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pa chaka chokondwerera zaka 50, mundawo udzabwezedwa kwa munthu amene adaugulitsayo, amene mtundawo unali wake ngati choloŵa chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pa chaka chokondwerera zaka makumi asanu, mundawo udzabwezedwa kwa munthu amene anawugulitsayo, amene malowo anali ake. Onani mutuwo |