Levitiko 27:23 - Buku Lopatulika23 pamenepo wansembeyo amwerengere mtengo wake wa kuyesa kwako kufikira chaka choliza lipenga; ndipo apereke kuyesa kwako tsiku lomwelo, chikhale chinthu chopatulikira Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 pamenepo wansembeyo amwerengere mtengo wake wa kuyesa kwako kufikira chaka choliza lipenga; ndipo apereke kuyesa kwako tsiku lomwelo, chikhale chinthu chopatulikira Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 wansembe aŵerenge mtengo wake kufikira pa chaka chokondwerera zaka 50. Tsono munthuyo apereke ndalama zokwanira mtengo wake pa tsikulo, kuti zikhale zopatulikira Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 wansembe atchule mtengo wake kufikira pa chaka chokondwerera zaka makumi asanu, ndipo munthuyo apereke ndalama zokwanira mtengo wake pa tsikulo monga ndalama zopatulika kwa Yehova. Onani mutuwo |