Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 27:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo akapatulira Yehova munda woti adaugula, wosati wogawako ku munda wakewake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo akapatulira Yehova munda woti adaugula, wosati wogawako ku munda wakewake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Munthu akapereka kwa Chauta munda umene waugula, umene suli chigawo cha choloŵa chake,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 “ ‘Ngati munthu apereka kwa Yehova munda umene anagula, umene si malo a makolo ake,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 27:22
5 Mawu Ofanana  

Ndipo muchipatule chaka cha makumi asanu, ndi kulalikira kwa onse okhala m'dzikomo kuti akhale aufulu; muchiyese chaka choliza lipenga; ndipo mubwerere munthu aliyense ku zakezake, ndipo mubwerere yense ku banja lake.


Mbale wako akasaukira chuma, nakagulitsa chakechake, pamenepo mombolo wake, mbale wake weniweni azidza, naombole chimene mbale wake anagulitsacho.


Munthu akapatula nyumba yake ikhale yopatulika kwa Yehova, wansembe aziiyesa mtengo wake, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga wansembeyo aiyesa, ikhale momwemo.


koma potuluka m'chaka choliza lipenga, mundawo ukhale wopatulikira Yehova, ngati munda woperekedwa chiperekere kwa Mulungu; ukhale wakewake wa wansembe.


pamenepo wansembeyo amwerengere mtengo wake wa kuyesa kwako kufikira chaka choliza lipenga; ndipo apereke kuyesa kwako tsiku lomwelo, chikhale chinthu chopatulikira Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa