Levitiko 27:20 - Buku Lopatulika20 Koma akapanda kuombola mundawo, kapena atagulitsa mundawo kwa munthu wina, suomboledwanso; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma akapanda kuombola mundawo, kapena atagulitsa mundawo kwa munthu wina, suomboledwanso; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma ngati safuna kuti aombole kapena ngati waugulitsa kwa munthu wina, mundawo sudzaombolekanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma ngati sawuwombola mundawo, kapena ngati waugulitsa kwa munthu wina, mundawo sudzawomboledwanso. Onani mutuwo |