Levitiko 27:17 - Buku Lopatulika17 Akapatula munda wake kuyambira chaka choliza lipenga, mundawo ukhale monga momwe unauyesera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Akapatula munda wake kuyambira chaka choliza lipenga, mundawo ukhale monga momwe unauyesera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Akapereka munda wake kuyambira pa chaka chokondwerera zaka 50, mtengo wake ukhale wathunthu monga momwe iwe udaikira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Ngati munthu apereka munda wake kuyambira chaka chokondwerera zaka makumi asanu, mtengo wake ukhale umene unakhazikitsidwa. Onani mutuwo |