Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 27:12 - Buku Lopatulika

12 ndipo wansembeyo aiyese mtengo wake, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga uiyesa wansembewe, momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 ndipo wansembeyo aiyese mtengo wake, ingakhale yokoma kapena yoipa; monga uiyesa wansembewe, momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ndipo wansembe atchule mtengo wake poona ngati njabwino kapena ai. Monga momwe iwe wansembe utchulire, mtengo udzakhala momwemo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 ndipo wansembeyo atchule mtengo wake poona ngati ndi yabwino kapena ndi yoyipa. Mtengo umene wansembe atchule ndiwo udzakhale mtengo wake.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 27:12
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yowasi anati kwa ansembe, Landirani ndalama zonse za zinthu zopatulika azibwera nazo kunyumba ya Yehova, ndizo ndalama za otha msinkhu, ndalama za munthu aliyense monga adamuyesa, ndi ndalama zimene yense azikumbuka m'mtima mwake kuti abwere nazo kunyumba ya Yehova.


Ndipo chikakhala cha nyama yodetsa, imene sabwera nayo ikhale chopereka cha Yehova, aike nyamayi pamaso pa wansembe;


Ndipo akaiombola ndithu, pamenepo aonjezepo limodzi la magawo asanu la mtengo wake.


pamenepo wansembeyo amwerengere mtengo wake wa kuyesa kwako kufikira chaka choliza lipenga; ndipo apereke kuyesa kwako tsiku lomwelo, chikhale chinthu chopatulikira Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa