Levitiko 27:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo chikakhala cha nyama yodetsa, imene sabwera nayo ikhale chopereka cha Yehova, aike nyamayi pamaso pa wansembe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo chikakhala cha nyama yodetsa, imene sabwera nayo ikhale chopereka cha Yehova, aike nyamayi pamaso pa wansembe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ikakhala nyama yonyansa, yonga imene siloledwa kuipereka ngati nsembe kwa Chauta, munthuyo abwere ndi nyamayo kwa wansembe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Ngati chimene anachitira lumbiro ndi nyama yodetsedwa, nyama imene siloledwa kuyipereka kukhala nsembe kwa Yehova, nyamayo abwere nayo kwa wansembe, Onani mutuwo |