Levitiko 27:10 - Buku Lopatulika10 Asaisinthe, yokoma m'malo mwa yoipa, kapena yoipa m'malo mwa yokoma; ndipo akasinthadi nyama m'malo mwa inzake, pamenepo iyo ndi yosinthikayo zikhale zopatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Asaisinthe, yokoma m'malo mwa yoipa, kapena yoipa m'malo mwa yokoma; ndipo akasinthadi nyama m'malo mwa inzake, pamenepo iyo ndi yosinthikayo zikhale zopatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Munthu asapereke ina m'malo mwake kapena kuisinthitsa ndi ina, asapereke yabwino m'malo mwa yoipa, kapena yoipa m'malo mwa yabwino. Ndipo akasinthitsa nyama ina ndi inzake, nyamayo pamodzi ndi inzake waisinthitsayo zikhala zopatulika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Munthu asasinthanitse ndi ina kapena kupereka ina yabwino mʼmalo mwa yoyipa, kapena yoyipa mʼmalo mwa yabwino. Ngati asinthitsa nyama ina mʼmalo mwa ina, nyamayo pamodzi ndi inzake wasinthitsayo zikhala zopatulika. Onani mutuwo |