Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 26:23 - Buku Lopatulika

23 Ndipo mukapanda kulangika nazo ndi kubwera kwa Ine, mukayenda motsutsana ndi Ine;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ndipo mukapanda kulangika nazo ndi kubwera kwa Ine, mukayenda motsutsana ndi Ine;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 “Mukapanda kubwerera kwa Ine nditakulangani chotere, ndipo mukachitabe zotsutsana ndi Ine,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 “ ‘Mukadzapanda kutembenukira kwa Ine ngakhale nditakulangani motere, ndi kumachitabe zotsutsana ndi Ine,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 26:23
9 Mawu Ofanana  

Ndi oyera mtima mudzadzionetsa woyera mtima; ndi otsutsatsutsa mudzadzionetsa wopotoza.


Pa woyera mtima mukhala woyera mtima; pa wotsutsatsutsa mukhala wotsutsana naye.


Ndapanda ana anu mwachabe; sanamvere kulanga; lupanga lanu ladya aneneri anu, monga mkango wakuononga.


Yehova Inu, maso anu sali pachoonadi kodi? Munawapanda iwo, koma sanaphwetekedwe mtima; munawatha iwo, koma akana kudzudzulidwa; alimbitsa nkhope zao koposa mwala; akana kubwera.


Monga mulembedwa m'chilamulo cha Mose choipa ichi chonse chatidzera; koma sitinapepese Yehova Mulungu wathu, ndi kubwera kuleka mphulupulu zathu, ndi kuchita mwanzeru m'choonadi chanu.


Ndipo mukayenda motsutsana nane, osalola kumvera Ine; ndidzakuonjezerani miliri kasanu ndi kawiri, monga mwa zochimwa zanu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa