Levitiko 25:4 - Buku Lopatulika4 koma chaka chachisanu ndi chiwiri chikhale Sabata lakupumula la dziko, Sabata la Yehova; usamabzala m'munda mwako, usamadzombola mipesa yako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 koma chaka chachisanu ndi chiwiri chikhale Sabata lakupumula la dziko, Sabata la Yehova; usamabzala m'munda mwako, usamadzombola mipesa yako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma chaka chachisanu ndi chiŵiri chikhale chaka chopumuza nthaka, chaka chopatulikira Chauta, ndipo musalime minda yanu kapena kuthenera mitengo yanu yamphesa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma chaka chachisanu ndi chiwiri ndi chaka choti nthaka ipume, chaka cha Sabata la Yehova. Musalime mʼminda yanu kapena kusadza mitengo yanu ya mpesa. Onani mutuwo |