Levitiko 25:3 - Buku Lopatulika3 Zaka zisanu ndi chimodzi ubzale m'munda mwako, ndi zaka zisanu ndi chimodzi udzombole mpesa zako, ndi kucheka zipatso zake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Zaka zisanu ndi chimodzi ubzale m'munda mwako, ndi zaka zisanu ndi chimodzi udzombole mphesa zako, ndi kucheka zipatso zake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pa zaka zisanu ndi chimodzi muzikalima minda yanu, ndipo muzikathenera mitengo yanu yamphesa ndi kuthyola zipatso zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pa zaka zisanu ndi chimodzi muzikalima minda yanu, ndipo kwa zaka zisanu ndi chimodzi muzikasadza mitengo yanu ya mpesa ndi kuthyola zipatso zake. Onani mutuwo |