Levitiko 24:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anamsunga m'kaidi, kuti awafotokozere m'mene anenere Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anamsunga m'kaidi, kuti awafotokozere m'mene anenere Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adamuika m'ndende mpaka atadziŵa kufuna kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Anamuyika mʼndende mpaka atadziwa bwino chofuna cha Yehova. Onani mutuwo |