Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 24:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo mwana wamwamuna wa mkazi Wachiisraele, atate wake ndiye Mwejipito, anatuluka mwa ana a Israele; ndi mwana wamwamuna wa mkazi Wachiisraeleyo analimbana naye munthu Mwisraele kuchigono;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo mwana wamwamuna wa mkazi Wachiisraele, atate wake ndiye Mwejipito, anatuluka mwa ana a Israele; ndi mwana wamwamuna wa mkazi Wachiisraeleyo analimbana naye munthu Mwisraele kuchigono;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Tsiku lina munthu wina amene mai wake anali Wachiisraele, koma bambo wake anali wa ku Ejipito, adapita kwa Aisraele ndipo adakangana ndi Mwisraele mmodzi ku mahema.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Tsiku lina munthu wina wamwamuna amene amayi ake anali Mwisraeli koma abambo ake anali Mwigupto anapita kwa Aisraeli ndipo anakangana ndi Mwisraeli wina ku msasa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 24:10
4 Mawu Ofanana  

Ndipo anthu ambiri osokonezeka anakwera nao; ndi nkhosa ndi ng'ombe, zoweta zambirimbiri.


ndipo mwana wamwamuna wa mkazi Wachiisraele anachitira Dzina mwano, natemberera; ndipo anadza naye kwa Mose. Dzina la mai wake ndiye Selomiti, mwana wa Dibiri, wa fuko la Dani.


Ndipo ukhale wa Aroni ndi ana ake, audye pamalo popatulika; pakuti auyese wopatulika kwambiri wochokera ku nsembe zamoto za Yehova; ndilo lemba losatha.


Ndipo anthu osokonezeka ali pakati pao anagwidwa nacho chilakolako; ndi ana a Israele omwe analiranso, nati, Adzatipatsa nyama ndani?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa