Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 23:5 - Buku Lopatulika

5 Mwezi woyamba, tsiku lakhumi ndi chinai la mweziwo, madzulo, pali Paska wa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Mwezi woyamba, tsiku lakhumi ndi chinai la mweziwo, madzulo, pali Paska wa Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 pa mwezi woyamba, tsiku la 14 la mweziwo, madzulo ake, ndi tsiku la Paska ya Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Chikondwerero cha Paska chiziyamba madzulo a tsiku la 14 la mwezi woyamba.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 23:5
14 Mawu Ofanana  

Uzisunga chikondwerero cha Mkate wopanda chotupitsa; masiku asanu ndi awiri uzidya mkate wopanda chotupitsa, monga ndinakuuza, nyengo yoikika, mwezi wa Abibu, pakuti m'menemo unatuluka mu Ejipito; koma asaoneke munthu pamaso panga opanda kanthu;


Mwezi woyamba, tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi, muzichita Paska, chikondwerero cha masiku asanu ndi awiri; audye mkate wopanda chotupitsa.


Ndipo tsiku loyamba la mkate wopanda chotupitsa, ophunzira anadza kwa Yesu, nati, Mufuna tikakonzere kuti Paska, kuti mukadye?


Ndipo tsiku loyamba la mikate yopanda chotupitsa, pamene amapha Paska, ophunzira ananena naye, Mufuna tinke kuti, tikakonze mkadyereko Paska?


Ndipo tsiku la mikate yopanda chotupitsa linafika, limene inayenera kuphedwa nsembe ya Paska.


Ndipo ana a Israele anamanga misasa ku Giligala; nachita Paska tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi, madzulo, m'zidikha za Yeriko.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa