Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 22:7 - Buku Lopatulika

7 Koma litalowa dzuwa, adzakhala woyera, ndi pambuyo pake adyeko zoyerazo, popeza ndizo chakudya chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Koma litalowa dzuwa, adzakhala woyera, ndi pambuyo pake adyeko zoyerazo, popeza ndizo chakudya chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Adzakhala woyeretsedwa dzuŵa litaloŵa, ndipo pambuyo pake adzatha kudyako zinthu zopatulikazo, poti zimenezo ndi chakudya chake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Munthuyo adzakhala woyeretsedwa pamene dzuwa lalowa, ndipo angathe kudya chopereka chopatulikacho popeza ndi chakudya chake.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 22:7
7 Mawu Ofanana  

Adye chakudya cha Mulungu wake, chopatulika kwambiri, ndi chopatulika;


munthu wokhudza chilichonse chotere adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo, ndipo asadye zinthu zopatulika, akapanda kusamba thupi lake ndi madzi.


Izi ndi zako pa zinthu zopatulika kwambiri, zosafika kumoto; zopereka zao zonse, ndi nsembe zao zonse zaufa, ndi nsembe zao zonse zauchimo, ndi nsembe zao zonse zopalamula, zimene andibwezera Ine, zikhale zopatulika kwambiri za iwe ndi za ana ako aamuna.


Kodi tilibe ulamuliro wa kudya ndi kumwa?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa