Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 22:5 - Buku Lopatulika

5 ndi aliyense wokhudza chinthu chokwawa chakudetsedwa nacho, kapenanso munthu amene akamdetsa nacho, chodetsa chake chilichonse;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 ndi aliyense wokhudza chinthu chokwawa chakudetsedwa nacho, kapenanso munthu amene akamdetsa nacho, chodetsa chake chilichonse;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mwina angathe kukhudza kachilombo kokwaŵa, kamene kangathe kumuipitsa, kapena kukhudza munthu amene angathe kumuipitsa mwa mtundu uliwonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 kapena kukhudza chilichonse chokwawa chomwe chimadetsa munthu, kapena kukhudza munthu amene angamudetse, kapenanso kukhudza kanthu kena kalikonse kodetsedwa.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 22:5
7 Mawu Ofanana  

Koma zokwawa zonse zakuuluka, za miyendo inai, muziyese zonyansa.


Ndipo ngati mkazi ali ndi nthenda yakukha, ndi kukha kwake nkwa mwazi m'thupi mwake, akhale padera masiku asanu ndi awiri; ndipo aliyense amkhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


Ndipo iye wakukhudza thupi la uyo wakukhayo atsuke zovala zake, nasambe m'madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


munthu wokhudza chilichonse chotere adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo, ndipo asadye zinthu zopatulika, akapanda kusamba thupi lake ndi madzi.


Ndipo chilichonse munthu wodetsedwa achikhudza chidzakhala chodetsedwa; ndi munthu wakuchikhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa