Levitiko 22:30 - Buku Lopatulika30 Idyedwe tsiku lomwelo; musamasiyako kufikira m'mawa; Ine ndine Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Idyedwe tsiku lomwelo; musamasiyako kufikira m'mawa; Ine ndine Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Muidye pa tsiku lomwelo, ndipo musaisiyeko mpaka m'maŵa. Ine ndine Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Muyidye pa tsiku lomwelo, wosasiyako ina mpaka mmawa. Ine ndine Yehova. Onani mutuwo |