Levitiko 22:24 - Buku Lopatulika24 Nyama yofula, kapena chophwanya kapena chosansantha, kapena chotudzula, kapena chodula, musamabwera nazo kwa Yehova; inde musamachita ichi m'dziko mwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Nyama yofula, kapena chopwanya kapena chosansantha, kapena chotudzula, kapena chodula, musamabwera nazo kwa Yehova; inde musamachita ichi m'dziko mwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Nyama iliyonse imene mavalo ake ali onyuka kapena otswanyika, kapena ong'ambika kapena oduka, musaipereke ngati nsembe kwa Chauta m'dziko mwanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Nyama iliyonse imene mavalo ake ndi onyuka kapena ophwanyika, ongʼambika kapena oduka, musamayipereke kwa Yehova mʼdziko lanu. Onani mutuwo |