Levitiko 22:16 - Buku Lopatulika16 ndi kuwasenzetsa mphulupulu yakuwapalamulitsa, pakudya iwo zopatulika zao; pakuti Ine ndine Yehova wakuwapatula. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 ndi kuwasenzetsa mphulupulu yakuwapalamulitsa, pakudya iwo zopatulika zao; pakuti Ine ndine Yehova wakuwapatula. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Asachimwitse ndi kupalamulitsa Aisraelewo pakuŵalola kudya zakudya zao zopatulika. Inetu ndine Chauta, amene ndimazipatula.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 ndipo asachimwitse ndi kupalamulitsa Aisraeli powalola kudya zakudya zawo zopatulika. Ine ndine Yehova amene ndimawayeretsa.’ ” Onani mutuwo |