Levitiko 22:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mwana wamkazi wa wansembe akakwatibwa ndi mlendo, asadyeko nsembe yokweza ya zinthu zopatulika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo mwana wamkazi wa wansembe akakwatibwa ndi mlendo, asadyeko nsembe yokweza ya zinthu zopatulika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Mwana wamkazi wa wansembe akakwatiwa ndi wapadera, asadyeko zopereka zopatulikazo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Mwana wamkazi wa wansembe amene wakwatiwa ndi munthu amene si wansembe, asadyeko nsembe zopatulikazo. Onani mutuwo |