Levitiko 22:11 - Buku Lopatulika11 Koma wansembe atakagula munthu ndi ndalama zake, iyeyu adyeko; ndi iwo amene anabadwa m'nyumba yake, adyeko mkate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma wansembe atakagula munthu ndi ndalama zake, iyeyu adyeko; ndi iwo amene anabadwa m'nyumba yake, adyeko mkate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma wansembe akagula kapolo ndi ndalama kuti akhale wake, kapoloyo angathe kudya nao zinthuzo. Ndipo onse amene abadwa m'nyumba mwa wansembe angathe kudyako chakudya chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma kapolo amene wagulidwa ndi ndalama kapena kubadwira mʼbanja la wansembe angathe kudya chakudya cha wansembeyo. Onani mutuwo |