Levitiko 21:7 - Buku Lopatulika7 Asadzitengere mkazi wachigololo, kapena woipsidwa; asatenge mkazi woti adamchotsa mwamuna wake; popeza apatulikira Mulungu wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Asadzitengere mkazi wachigololo, kapena woipsidwa; asatenge mkazi woti adamchotsa mwamuna wake; popeza apatulikira Mulungu wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Asakwatire mkazi wachiwerewere kapena mkazi amene wadziipitsa, ndiponso asakwatire mkazi amene mwamuna wake wamsudzula, pakuti wansembe ndi woyera pamaso pa Mulungu wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 “ ‘Asakwatire akazi amene adzidetsa ndi chiwerewere kapena akazi amene amuna awo awasudzula, chifukwa ansembe ndi oyera pamaso pa Mulungu wawo. Onani mutuwo |