Levitiko 21:4 - Buku Lopatulika4 Akakhala mwini banja pakati pa anthu a mtundu wake, asadzidetse, ndi kudziipsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Akakhala mwini banja pakati pa anthu a mtundu wake, asadzidetse, ndi kudziipsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Wansembe asadziipitse pa imfa ya munthu amene wakwatira naye ku banja limodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Koma wansembe asadzidetse chifukwa cha anthu amene ali nawo pa ubale obwera chifukwa cha ukwati. Onani mutuwo |