Levitiko 21:3 - Buku Lopatulika3 ndi chifukwa cha mlongo wake weniweni, akakhala namwali wosakhala naye mwamuna, nkuloleka adzidetse chifukwa cha iwowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndi chifukwa cha mlongo wake weniweni, akakhala namwali wosakhala naye mwamuna, nkuloleka adzidetse chifukwa cha iwowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 kapena mlongo wake wosakwatiwa amene amakhala pafupi naye, poti chikhalire alibe mwamuna. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 kapena mlongo wake wosakwatiwa amene amadalira iye chifukwa sanakwatiwe. Iye akhoza kudzidetsa pokhudza thupi lakufa la mchemwali wake wosakwatiwa yekha. Onani mutuwo |