Levitiko 21:2 - Buku Lopatulika2 koma chifukwa cha abale ake enieni ndiwo, mai wake, ndi atate wake, ndi mwana wake wamwamuna, ndi mwana wake wamkazi, ndi mbale wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 koma chifukwa cha abale ake enieni ndiwo, mai wake, ndi atate wake, ndi mwana wake wamwamuna, ndi mwana wake wamkazi, ndi mbale wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma angathe kukhudza mai wake, bambo wake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma akhoza kukhudza thupi lakufa la amayi ake, abambo ake, mwana wake wamwamuna, mwana wake wamkazi, mchimwene wake, Onani mutuwo |