Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 21:18 - Buku Lopatulika

18 Pakuti munthu aliyense wokhala nacho chilema, asayandikize; wakhungu, kapena wotsimphina, kapena wopunduka mphuno, kapena wamkulu chiwalo,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Pakuti munthu aliyense wokhala nacho chilema, asayandikize; wakhungu, kapena wotsimphina, kapena wopunduka mphuno, kapena wamkulu chiwalo,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Munthu aliyense wachilema sayenera kusendera pafupi, monga munthu wakhungu kapena wopunduka miyendo, munthu wopunduka nkhope kapena wokhala ndi chiwalo china chachitali dziŵi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Munthu aliyense wachilema motere: munthu wakhungu kapena wolumala miyendo, munthu wolumala nkhope kapena waziwalo zambiri,

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 21:18
9 Mawu Ofanana  

Alonda ake ali akhungu, iwo onse ali opanda nzeru; iwo onse ali agalu achete, osatha kuuwa; kungolota, kugona pansi, kukonda kugona tulo.


kapena munthu wopunduka phazi kapena wopunduka dzanja,


Inu akhungu, pakuti choposa nchiti, mtulo kodi, kapena guwa la nsembe limene liyeretsa mtulowo?


Kuyeneranso kuti iwo akunja adzakhoza kumchitira umboni wabwino; kuti ungamgwere mtonzo, ndi msampha wa mdierekezi.


Pakuti alipo ambiri osamvera mau, olankhula zopanda pake, ndi onyenga, makamaka iwo akumdulidwe,


Pakuti woyang'anira ayenera kukhala wopanda chilema, ngati mdindo wa Mulungu; wosati waliuma, wosapsa mtima msanga, wosati wachiwawa, wopanda ndeu, wosati wa chisiriro chonyansa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa