Levitiko 20:15 - Buku Lopatulika15 Mwamuna akagona ndi nyama amuphe ndithu; muiphenso nyamayi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Mwamuna akagona ndi nyama amuphe ndithu; muiphenso nyamayi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mwamuna akagona ndi nyama, ayenera kuphedwa, ndipo nyamayo muiphenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 “ ‘Ngati mwamuna agonana ndi nyama, iye ayenera kuphedwa, ndipo muyeneranso kupha nyamayo. Onani mutuwo |