Levitiko 19:9 - Buku Lopatulika9 Pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Pamene mukolola m'minda mwanu, musakolole munda wanu mpaka m'malire mwenimweni, ndipo musatolenso khunkha lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “ ‘Pamene mukolola zinthu mʼmunda mwanu musakolole mpaka mʼmphepete mwa munda, ndipo musatole khunkha lake. Onani mutuwo |