Levitiko 19:6 - Buku Lopatulika6 Tsiku lomwelo mwaipha, ndi m'mawa mwake muidye; ngati katsalirako kanthu tsiku lachitatu, muzikatentha ndi moto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Tsiku lomwelo mwaipha, ndi m'mawa mwake muidye; ngati katsalirako kanthu tsiku lachitatu, muzikatentha ndi moto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Muidye tsiku lomwe mwaiperekalo, kapena m'maŵa mwake, koma zotsalako mpaka pa tsiku lachitatu muzitenthe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nsembe izidyedwa tsiku lomwe mwayiperekalo kapena mmawa mwake. Chilichonse chotsala mpaka tsiku lachitatu chiyenera kutenthedwa. Onani mutuwo |