Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Levitiko 19:24 - Buku Lopatulika

24 Koma chaka chachinai zipatso zake zonse zikhale zopatulika, za kumlemekeza nazo Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Koma chaka chachinai zipatso zake zonse zikhale zopatulika, za kumlemekeza nazo Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Pa chaka chachinai, zipatso zonse zidzakhala zopatulikira Chauta ngati nsembe yomtamandira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Chaka chachinayi, zipatso zake zonse zidzakhala zopatulika, ndipo zidzakhala chopereka cha matamando kwa Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Levitiko 19:24
7 Mawu Ofanana  

Lemekeza Yehova ndi chuma chako, ndi zinthu zako zonse zoyambirira kucha;


Ndipo mukadzalowa m'dzikomo, ndi kubzala mitengo ya mitundumitundu ikhale ya chakudya, muziyese zipatso zao monga kusadulidwa kwao; zaka zitatu muziyese zosadulidwa; zisadyedwa.


Chaka chachisanu muzidya zipatso zake, kuti zobala zake zikuchulukireni inu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.


Zipatso zoyamba za tirigu wanu, za vinyo wanu, ndi za mafuta anu ndi ubweya woyamba kuusenga, muwapatse izi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa