Levitiko 19:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo wansembe achite chomtetezera ndi nkhosa yamphongo ya nsembe yopalamula pamaso pa Yehova, chifukwa cha kuchimwa adachimwaku; ndipo adzakhululukidwa chifukwa cha kuchimwa kwake adachimwaku. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo wansembe achite chomtetezera ndi nkhosa yamphongo ya nsembe yopalamula pamaso pa Yehova, chifukwa cha kuchimwa adachimwaku; ndipo adzakhululukidwa chifukwa cha kuchimwa kwake adachimwaku. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Wansembe achite mwambo wopepesera machimo a munthuyo ndi nkhosa yamphongo ya nsembe yopepesera kupalamulayo pamaso pa Chauta, chifukwa cha tchimo limene munthuyo adachita, ndipo tchimo adachitalo lidzakhululukidwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 ndipo wansembe achite nayo mwambo wopepesera chifukwa cha kupalamula kumene anachita pamaso pa Yehova. Akatero tchimo lake lidzakhululukidwa. Onani mutuwo |